Nyimbo ya Solomo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Wokondedwa wangawe,+ ndiwe wokongola ngati Tiriza,*+Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+Ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera.+ Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:4 Nsanja ya Olonda,11/15/2006, ptsa. 19-2011/15/1987, tsa. 25
4 “Wokondedwa wangawe,+ ndiwe wokongola ngati Tiriza,*+Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+Ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera.+