Nyimbo ya Solomo 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Kodi mkazi amene akuwala* ngati mʼbandakuchayu ndi ndani,Amene ndi wokongola ngati mwezi wathunthu,Wosadetsedwa ngati kuwala kwa dzuwa,Wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera?’”+
10 ‘Kodi mkazi amene akuwala* ngati mʼbandakuchayu ndi ndani,Amene ndi wokongola ngati mwezi wathunthu,Wosadetsedwa ngati kuwala kwa dzuwa,Wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera?’”+