Nyimbo ya Solomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Bwerera, bwerera iwe Msulami! Bwerera, bwereraKuti tione kukongola kwako!” “Nʼchifukwa chiyani mukuyangʼanitsitsa Msulami?”+ “Iye ali ngati gule wa magulu awiri a anthu.”* Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:13 Nsanja ya Olonda,11/15/2006, tsa. 20
13 “Bwerera, bwerera iwe Msulami! Bwerera, bwereraKuti tione kukongola kwako!” “Nʼchifukwa chiyani mukuyangʼanitsitsa Msulami?”+ “Iye ali ngati gule wa magulu awiri a anthu.”*