-
Nyimbo ya Solomo 7:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mchombo wako uli ngati mbale yolowa.
Vinyo wosakaniza bwino asasowepo.
Mimba yako ili ngati mulu wa tirigu,
Wozunguliridwa ndi maluwa.
-