Nyimbo ya Solomo 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Undiike pamtima pako ngati chidindo,Ndiponso undiike ngati chidindo padzanja lako,Chifukwa mofanana ndi Manda,* chikondi sichigonja,+Ndipo chimafuna kudzipereka ndi mtima wonse. Chikondi chimenechi chili ngati malawi a moto. Chikondicho ndi lawi la Ya.*+ Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2023, tsa. 20 Nsanja ya Olonda,1/15/2015, tsa. 295/15/2012, tsa. 411/15/2006, tsa. 2011/15/1987, tsa. 25
6 Undiike pamtima pako ngati chidindo,Ndiponso undiike ngati chidindo padzanja lako,Chifukwa mofanana ndi Manda,* chikondi sichigonja,+Ndipo chimafuna kudzipereka ndi mtima wonse. Chikondi chimenechi chili ngati malawi a moto. Chikondicho ndi lawi la Ya.*+
8:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2023, tsa. 20 Nsanja ya Olonda,1/15/2015, tsa. 295/15/2012, tsa. 411/15/2006, tsa. 2011/15/1987, tsa. 25