Yesaya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani inu okhala kumwamba, ndipo tcherani khutu inu okhala padziko lapansi,+Chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana nʼkuwasamalira kuti akule,+Koma iwo andipandukira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Yesaya 1, ptsa. 11-12
2 Imvani inu okhala kumwamba, ndipo tcherani khutu inu okhala padziko lapansi,+Chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana nʼkuwasamalira kuti akule,+Koma iwo andipandukira.+