Yesaya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dziko lanu lawonongedwa. Mizinda yanu yawotchedwa ndi moto. Alendo akudya zokolola zochokera munthaka yanu, inu mukuona.+ Lawonongedwa ngati dziko limene lalandidwa ndi adani.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Yesaya 1, ptsa. 17-18
7 Dziko lanu lawonongedwa. Mizinda yanu yawotchedwa ndi moto. Alendo akudya zokolola zochokera munthaka yanu, inu mukuona.+ Lawonongedwa ngati dziko limene lalandidwa ndi adani.+