Yesaya 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana wamkazi wa Ziyoni* wasiyidwa ngati msasa mʼmunda wa mpesa,Ngati chisimba* mʼmunda wa nkhaka,Ndiponso ngati mzinda umene wazunguliridwa ndi adani.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Nsanja ya Olonda,12/1/2006, ptsa. 8-9 Yesaya 1, ptsa. 18-19
8 Mwana wamkazi wa Ziyoni* wasiyidwa ngati msasa mʼmunda wa mpesa,Ngati chisimba* mʼmunda wa nkhaka,Ndiponso ngati mzinda umene wazunguliridwa ndi adani.+