Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino, muzichita chilungamo,+Dzudzulani munthu wopondereza ena,Tetezani ufulu wa mwana wamasiye,Ndipo muteteze mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:17 Yesaya 1, ptsa. 26, 27-28 Nsanja ya Olonda,8/1/1998, tsa. 14
17 Phunzirani kuchita zabwino, muzichita chilungamo,+Dzudzulani munthu wopondereza ena,Tetezani ufulu wa mwana wamasiye,Ndipo muteteze mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+