Yesaya 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Akalonga ako ndi osamva ndipo amagwirizana ndi anthu akuba.+ Aliyense wa iwo amakonda ziphuphu ndipo amalakalaka kupatsidwa mphatso.+ Mwana wamasiye samuweruza mwachilungamo,Ndipo ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye safuna kuuweruza.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:23 Yesaya 1, tsa. 31
23 Akalonga ako ndi osamva ndipo amagwirizana ndi anthu akuba.+ Aliyense wa iwo amakonda ziphuphu ndipo amalakalaka kupatsidwa mphatso.+ Mwana wamasiye samuweruza mwachilungamo,Ndipo ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye safuna kuuweruza.+