Yesaya 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Mulungu Wamphamvu wa Isiraeli, wanena kuti: “Eya! Ndidzachotsa adani anga pamaso panga,Ndipo ndidzabwezera adani anga.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:24 Yesaya 1, tsa. 32
24 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Mulungu Wamphamvu wa Isiraeli, wanena kuti: “Eya! Ndidzachotsa adani anga pamaso panga,Ndipo ndidzabwezera adani anga.+