Yesaya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo,Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Yesaya 1, ptsa. 50-51
8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo,Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.