Yesaya 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yerusalemu wapunthwaNdipo Yuda wagwa,Chifukwa zonena ndi zochita zawo zikutsutsana ndi Yehova.Iwo achita zinthu zomupandukira pamaso pake polemekezeka.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:8 Yesaya 1, tsa. 57
8 Yerusalemu wapunthwaNdipo Yuda wagwa,Chifukwa zonena ndi zochita zawo zikutsutsana ndi Yehova.Iwo achita zinthu zomupandukira pamaso pake polemekezeka.*+