Yesaya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uzani anthu olungama kuti zidzawayendera bwino,Iwo adzalandira mphoto chifukwa cha zimene akuchita.*+
10 Uzani anthu olungama kuti zidzawayendera bwino,Iwo adzalandira mphoto chifukwa cha zimene akuchita.*+