Yesaya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Amene amayangʼanira anthu anga akamagwira ntchito, akuwachitira nkhanza,Ndipo akazi ndi amene akuwalamulira. Inu anthu anga, atsogoleri anu akukusocheretsani,Ndipo achititsa kuti musadziwe njira yoyenera kutsatira.+
12 Amene amayangʼanira anthu anga akamagwira ntchito, akuwachitira nkhanza,Ndipo akazi ndi amene akuwalamulira. Inu anthu anga, atsogoleri anu akukusocheretsani,Ndipo achititsa kuti musadziwe njira yoyenera kutsatira.+