Yesaya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti ana aakazi a Ziyoni ndi onyada,Akuyenda mwamatama,*Amakopa amuna ndi maso awo, nʼkumayenda modzigomera,Komanso amapanga phokoso chifukwa cha zodzikongoletsera zimene amavala mʼmiyendo yawo, Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Yesaya 1, ptsa. 58-59
16 Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti ana aakazi a Ziyoni ndi onyada,Akuyenda mwamatama,*Amakopa amuna ndi maso awo, nʼkumayenda modzigomera,Komanso amapanga phokoso chifukwa cha zodzikongoletsera zimene amavala mʼmiyendo yawo, Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Yesaya 1, ptsa. 58-59