Yesaya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Malo olowera mumzinda adzalira ndipo adzamva chisoni,+Mzindawo udzakhala padothi penipeni ndipo udzakhala wopanda chilichonse.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:26 Yesaya 1, tsa. 60
26 Malo olowera mumzinda adzalira ndipo adzamva chisoni,+Mzindawo udzakhala padothi penipeni ndipo udzakhala wopanda chilichonse.”+