Yesaya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikufuna ndimuimbire nyimbo wokondedwa wangaNyimbo yonena za munthu amene ndimamukonda ndiponso munda wake wa mpesa.+ Wokondedwa wanga anali ndi munda wa mpesa pamalo achonde mʼmbali mwa phiri. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Nsanja ya Olonda,6/15/2006, tsa. 17 Yesaya 1, ptsa. 73-74, 76
5 Ndikufuna ndimuimbire nyimbo wokondedwa wangaNyimbo yonena za munthu amene ndimamukonda ndiponso munda wake wa mpesa.+ Wokondedwa wanga anali ndi munda wa mpesa pamalo achonde mʼmbali mwa phiri.