Yesaya 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsoka kwa anthu amene akuwonjezera nyumba zina panyumba zawo,+Ndiponso amene akuwonjezera minda ina kuminda yawo,+Mpaka malo onse kutha,Ndipo iwo ayamba kukhala okhaokha mʼdzikoli. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:8 Yesaya 1, ptsa. 79-80
8 Tsoka kwa anthu amene akuwonjezera nyumba zina panyumba zawo,+Ndiponso amene akuwonjezera minda ina kuminda yawo,+Mpaka malo onse kutha,Ndipo iwo ayamba kukhala okhaokha mʼdzikoli.