Yesaya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba walumbira ine ndikumvaKuti nyumba zambiri, ngakhale kuti ndi zikuluzikulu komanso zokongola,Zidzakhala chinthu chodabwitsa kwambiriNdipo simudzakhala aliyense.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:9 Yesaya 1, ptsa. 79-80
9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba walumbira ine ndikumvaKuti nyumba zambiri, ngakhale kuti ndi zikuluzikulu komanso zokongola,Zidzakhala chinthu chodabwitsa kwambiriNdipo simudzakhala aliyense.+