Yesaya 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa maekala 10* a munda wa mpesa adzatulutsa mtsuko* umodzi wokha wa vinyo,Ndipo mbewu zokwana muyezo umodzi wa homeri* zidzatulutsa zokolola zokwana muyezo umodzi wokha wa efa.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:10 Yesaya 1, ptsa. 79-80
10 Chifukwa maekala 10* a munda wa mpesa adzatulutsa mtsuko* umodzi wokha wa vinyo,Ndipo mbewu zokwana muyezo umodzi wa homeri* zidzatulutsa zokolola zokwana muyezo umodzi wokha wa efa.*+