Yesaya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa anthu amene amadzuka mʼmamawa kwambiri kuti amwe mowa,+Amene amakhala akumwabe mpaka madzulo kutada, moti vinyo amawaledzeretsa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:11 Yesaya 1, tsa. 81
11 Tsoka kwa anthu amene amadzuka mʼmamawa kwambiri kuti amwe mowa,+Amene amakhala akumwabe mpaka madzulo kutada, moti vinyo amawaledzeretsa.