Yesaya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anthu anga adzapita ku ukapolo kudziko linaChifukwa chosadziwa zinthu.+Anthu awo olemekezeka adzakhala ndi njala,+Ndipo anthu awo onse adzakhala ndi ludzu.
13 Choncho anthu anga adzapita ku ukapolo kudziko linaChifukwa chosadziwa zinthu.+Anthu awo olemekezeka adzakhala ndi njala,+Ndipo anthu awo onse adzakhala ndi ludzu.