Yesaya 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsoka kwa amene akunena kuti chabwino nʼchoipa ndipo choipa nʼchabwino,+Amene akuika mdima mʼmalo mwa kuwala ndi kuwala mʼmalo mwa mdima,Amene akuika zowawa mʼmalo mwa zotsekemera ndi zotsekemera mʼmalo mwa zowawa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:20 Nsanja ya Olonda,3/1/2002, tsa. 98/1/2001, ptsa. 8-9 Yesaya 1, ptsa. 82-84
20 Tsoka kwa amene akunena kuti chabwino nʼchoipa ndipo choipa nʼchabwino,+Amene akuika mdima mʼmalo mwa kuwala ndi kuwala mʼmalo mwa mdima,Amene akuika zowawa mʼmalo mwa zotsekemera ndi zotsekemera mʼmalo mwa zowawa.