Yesaya 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsoka kwa anthu amene amaweruza kuti woipa alibe mlandu chifukwa choti alandira chiphuphu,+Ndiponso kwa amene amalephera kuweruza anthu olungama mwachilungamo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:23 Yesaya 1, tsa. 84
23 Tsoka kwa anthu amene amaweruza kuti woipa alibe mlandu chifukwa choti alandira chiphuphu,+Ndiponso kwa amene amalephera kuweruza anthu olungama mwachilungamo.+