Yesaya 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye waikira chizindikiro mtundu wakutali.+Wauimbira likhweru kuti ubwere kuchokera kumapeto kwa dziko lapansi.+Ndipotu mtunduwo ukubwera mofulumira kwambiri.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:26 Yesaya 1, ptsa. 84-86
26 Iye waikira chizindikiro mtundu wakutali.+Wauimbira likhweru kuti ubwere kuchokera kumapeto kwa dziko lapansi.+Ndipotu mtunduwo ukubwera mofulumira kwambiri.+