-
Yesaya 5:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Ziboda za mahatchi awo nʼzolimba ngati mwala wa nsangalabwi,
Ndipo mawilo a magaleta awo ali ngati mphepo yamkuntho.+
-