-
Yesaya 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iye anakhudza pakamwa panga nʼkunena kuti:
“Taona! Khalali lakhudza milomo yako.
Zolakwa zako zachotsedwa,
Ndipo tchimo lako laphimbidwa.”
-