Yesaya 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mʼdzikolo mudzakhalabe chakhumi ndipo chidzawotchedwanso ngati mtengo waukulu, ndiponso ngati chimtengo chachikulu, chimene chikadulidwa pamatsala chitsa. Mbewu* yopatulika idzakhala chitsa chake.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:13 Yesaya 1, ptsa. 97-98, 99-100 Nsanja ya Olonda,10/15/1987, ptsa. 18-19
13 Koma mʼdzikolo mudzakhalabe chakhumi ndipo chidzawotchedwanso ngati mtengo waukulu, ndiponso ngati chimtengo chachikulu, chimene chikadulidwa pamatsala chitsa. Mbewu* yopatulika idzakhala chitsa chake.”