Yesaya 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yehova anauza Yesaya kuti: “Pita ukakumane ndi Ahazi. Upite ndi mwana wako Seari-yasubu.*+ Ukakumane naye kumapeto kwa ngalande yochokera kudziwe lakumtunda,+ mʼmphepete mwa msewu waukulu wopita kumalo a wochapa zovala. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:3 Yesaya 1, ptsa. 102-104
3 Kenako Yehova anauza Yesaya kuti: “Pita ukakumane ndi Ahazi. Upite ndi mwana wako Seari-yasubu.*+ Ukakumane naye kumapeto kwa ngalande yochokera kudziwe lakumtunda,+ mʼmphepete mwa msewu waukulu wopita kumalo a wochapa zovala.