Yesaya 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukamuuze kuti, ‘Mtima wako ukhale mʼmalo. Usachite mantha ndipo usataye mtima chifukwa cha zitsa ziwirizi zimene zikungofuka utsi, chifukwa cha mkwiyo waukulu wa Rezini mfumu ya Siriya ndiponso mkwiyo wa mwana wa Remaliya.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:4 Nsanja ya Olonda,12/1/2006, tsa. 9 Yesaya 1, tsa. 104
4 Ukamuuze kuti, ‘Mtima wako ukhale mʼmalo. Usachite mantha ndipo usataye mtima chifukwa cha zitsa ziwirizi zimene zikungofuka utsi, chifukwa cha mkwiyo waukulu wa Rezini mfumu ya Siriya ndiponso mkwiyo wa mwana wa Remaliya.+