Yesaya 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa likulu la Siriya ndi Damasiko,Ndipo mfumu ya Damasiko ndi Rezini. Zaka 65 zisanathe,Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa ndipo sadzakhalanso mtundu wa anthu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:8 Nsanja ya Olonda,12/1/2006, tsa. 9 Yesaya 1, ptsa. 105-106
8 Chifukwa likulu la Siriya ndi Damasiko,Ndipo mfumu ya Damasiko ndi Rezini. Zaka 65 zisanathe,Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa ndipo sadzakhalanso mtundu wa anthu.+