Yesaya 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mwanayo asanafike podziwa kukana choipa ndi kusankha chabwino, mayiko a mafumu awiri amene ukuchita nawo manthawo, adzakhala atasiyidwiratu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:16 Yesaya 1, ptsa. 107-108
16 Mwanayo asanafike podziwa kukana choipa ndi kusankha chabwino, mayiko a mafumu awiri amene ukuchita nawo manthawo, adzakhala atasiyidwiratu.+