Yesaya 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova adzabweretsera iweyo, anthu ako komanso nyumba ya bambo ako nthawi yovuta imene sinakhaleponso kuyambira tsiku limene Efuraimu anapatukana ndi Yuda.+ Iye adzakubweretserani mfumu ya Asuri.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:17 Yesaya 1, tsa. 109
17 Yehova adzabweretsera iweyo, anthu ako komanso nyumba ya bambo ako nthawi yovuta imene sinakhaleponso kuyambira tsiku limene Efuraimu anapatukana ndi Yuda.+ Iye adzakubweretserani mfumu ya Asuri.+