Yesaya 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo zonse zidzabwera nʼkudzatera mʼzigwa zokhala* ndi maphompho, mʼmingʼalu ya mʼmatanthwe, pazitsamba zonse zaminga ndiponso mʼmalo onse omwetserapo ziweto. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:19 Yesaya 1, tsa. 110
19 Ndipo zonse zidzabwera nʼkudzatera mʼzigwa zokhala* ndi maphompho, mʼmingʼalu ya mʼmatanthwe, pazitsamba zonse zaminga ndiponso mʼmalo onse omwetserapo ziweto.