-
Yesaya 7:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Tsiku limenelo, pamalo alionse pamene panali mitengo ya mpesa 1,000, yokwana ndalama zasiliva 1,000, padzangokhala zitsamba zaminga ndi udzu.
-