-
Yesaya 7:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Anthu azidzapita kumeneko atanyamula mivi ndi mauta, chifukwa mʼdziko lonselo mudzamera zitsamba zaminga ndi udzu.
-