-
Yesaya 7:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndipo mʼmapiri onse amene anthu ankalambulako ndi makasu, sudzapitakonso chifukwa choopa zitsamba zaminga ndi udzu. Malowo adzakhala odyetserako ngʼombe zamphongo ndiponso oti nkhosa zizipondapondapo.”
-