Yesaya 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ndinagona ndi mneneri wamkazi* ndipo anakhala woyembekezera. Pambuyo pake anabereka mwana wamwamuna.+ Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Umupatse dzina lakuti Maheri-salala-hasi-bazi, Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Nsanja ya Olonda,11/15/2013, ptsa. 16-17 Yesaya 1, ptsa. 8, 112
3 Kenako ndinagona ndi mneneri wamkazi* ndipo anakhala woyembekezera. Pambuyo pake anabereka mwana wamwamuna.+ Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Umupatse dzina lakuti Maheri-salala-hasi-bazi,