Yesaya 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa mwanayo asanadziwe kuitana kuti, ‘Ababa!’ kapena ‘Amama!’ chuma cha ku Damasiko ndi katundu wolandidwa ku Samariya zidzatengedwa nʼkupita nazo kwa mfumu ya Asuri.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:4 Yesaya 1, tsa. 112
4 chifukwa mwanayo asanadziwe kuitana kuti, ‘Ababa!’ kapena ‘Amama!’ chuma cha ku Damasiko ndi katundu wolandidwa ku Samariya zidzatengedwa nʼkupita nazo kwa mfumu ya Asuri.”+