Yesaya 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi amene uyenera kumuona kuti ndi woyera,+Ndi amene uyenera kumuopa,Ndipo ndi amene uyenera kumulemekeza.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:13 Yesaya 1, tsa. 115
13 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi amene uyenera kumuona kuti ndi woyera,+Ndi amene uyenera kumuopa,Ndipo ndi amene uyenera kumulemekeza.”+