Yesaya 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo aliyense adzadutsa mʼdzikolo akuzunzika ndiponso ali ndi njala.+ Chifukwa chakuti ali ndi njala komanso wakwiya, adzatukwana mfumu yake ndi Mulungu wake ndipo azidzayangʼana kumwamba. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:21 Nsanja ya Olonda,8/15/2013, tsa. 11 Yesaya 1, ptsa. 123-124
21 Ndipo aliyense adzadutsa mʼdzikolo akuzunzika ndiponso ali ndi njala.+ Chifukwa chakuti ali ndi njala komanso wakwiya, adzatukwana mfumu yake ndi Mulungu wake ndipo azidzayangʼana kumwamba.