-
Yesaya 9:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Chifukwa kuipa kwayaka ngati moto,
Ndipo kukupsereza zitsamba zaminga ndi udzu.
Kuipako kudzayatsa zitsamba zowirira zamʼnkhalango,
Ndipo utsi wa mitengoyo udzakwera mʼmwamba kuti tolo!
-