-
Yesaya 9:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Munthu adzacheka zimene zili kumbali yakumanja
Koma adzakhalabe ndi njala.
Ndipo munthu adzadya zimene zili kumanzere kwake
Koma sadzakhuta.
Aliyense adzadya mnofu wa dzanja lake,
-