Yesaya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Manase adzadya Efuraimu,Ndipo Efuraimu adzadya Manase. Awiriwa adzaukira Yuda limodzi.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere,Koma dzanja lake lidakali lotambasula kuti awalange.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:21 Yesaya 1, ptsa. 134, 139-140
21 Manase adzadya Efuraimu,Ndipo Efuraimu adzadya Manase. Awiriwa adzaukira Yuda limodzi.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere,Koma dzanja lake lidakali lotambasula kuti awalange.+