Yesaya 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuti asamvetsere mlandu wa anthu osaukaNdiponso kuti asachitire chilungamo anthu onyozeka amene ali pakati pa anthu anga.+Amalanda katundu wa akazi amasiyeKomanso katundu wa ana amasiye.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:2 Yesaya 1, ptsa. 140-142
2 Kuti asamvetsere mlandu wa anthu osaukaNdiponso kuti asachitire chilungamo anthu onyozeka amene ali pakati pa anthu anga.+Amalanda katundu wa akazi amasiyeKomanso katundu wa ana amasiye.+