Yesaya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye wanena kuti: “Eya! Onani Msuri,+Iye ndi ndodo yosonyezera mkwiyo wanga+Ndipo ndigwiritsa ntchito chikwapu chimene chili mʼdzanja lake popereka chilango. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:5 Yesaya 1, ptsa. 144-146, 152-153
5 Iye wanena kuti: “Eya! Onani Msuri,+Iye ndi ndodo yosonyezera mkwiyo wanga+Ndipo ndigwiritsa ntchito chikwapu chimene chili mʼdzanja lake popereka chilango.