Yesaya 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzamutumiza kuti akalimbane ndi mtundu wopanduka,+Kuti akalimbane ndi anthu amene andikwiyitsa.Ndidzamulamula kuti akalande zinthu zambiriNdiponso kuti akapondeponde anthu ngati matope amumsewu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:6 Yesaya 1, ptsa. 144-146, 152-153
6 Ndidzamutumiza kuti akalimbane ndi mtundu wopanduka,+Kuti akalimbane ndi anthu amene andikwiyitsa.Ndidzamulamula kuti akalande zinthu zambiriNdiponso kuti akapondeponde anthu ngati matope amumsewu.+