-
Yesaya 10:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Mofanana ndi munthu amene akupisa dzanja lake mʼchisa,
Dzanja langa lidzalanda zinthu zofunika za anthu a mitundu ina.
Ngati mmene munthu amasonkhanitsira mazira amene asiyidwa,
Ine ndidzasonkhanitsa zinthu zonse zapadziko lapansi.
Palibe aliyense amene adzakupize mapiko ake kapena kutsegula pakamwa pake kapenanso kulira ngati mbalame.’”
-