Yesaya 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwambaAdzachititsa kuti anthu ake* onenepa awonde,+Ndipo pansi pa ulemerero wake adzayatsapo moto.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Yesaya 1, ptsa. 149-150
16 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwambaAdzachititsa kuti anthu ake* onenepa awonde,+Ndipo pansi pa ulemerero wake adzayatsapo moto.+